Ekisodo 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Utengenso kasiya* masekeli 500 ofanana ndi masekeli akumalo oyera*+ komanso hini* imodzi ya mafuta a maolivi.
24 Utengenso kasiya* masekeli 500 ofanana ndi masekeli akumalo oyera*+ komanso hini* imodzi ya mafuta a maolivi.