Ekisodo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakanizidwa mwaluso.*+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.
25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakanizidwa mwaluso.*+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.