Ekisodo 30:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza.+ Usakanize zonunkhiritsa zimenezi mwaluso,* uthire mchere,+ zikhale zoyera ndi zopatulika.
35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza.+ Usakanize zonunkhiritsa zimenezi mwaluso,* uthire mchere,+ zikhale zoyera ndi zopatulika.