Ekisodo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuwonjezera pamenepo ine ndaika Oholiabu+ mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani kuti athandize Bezaleli. Komanso ndaika nzeru mumtima wa anthu onse amene ali ndi luso,* kuti apange zonse zimene ndakulamulazi:+
6 Kuwonjezera pamenepo ine ndaika Oholiabu+ mwana wamwamuna wa Ahisama wa fuko la Dani kuti athandize Bezaleli. Komanso ndaika nzeru mumtima wa anthu onse amene ali ndi luso,* kuti apange zonse zimene ndakulamulazi:+