Ekisodo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzisunga Sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Aliyense wosatsatira lamulo lokhudza sabata ayenera kuphedwa ndithu. Munthu aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
14 Muzisunga Sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Aliyense wosatsatira lamulo lokhudza sabata ayenera kuphedwa ndithu. Munthu aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+