Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwa ndi chala cha Mulungu.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:18 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 5
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwa ndi chala cha Mulungu.+