Ekisodo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mose ali mʼphirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Choncho anthuwo anasonkhana kwa Aroni nʼkumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.” Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:1 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, tsa. 11
32 Mose ali mʼphirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Choncho anthuwo anasonkhana kwa Aroni nʼkumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.”