Ekisodo 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Aroni anawauza kuti: “Tengani ndolo zagolide+ zimene avala akazi anu, ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mubwere nazo kwa ine.”
2 Ndiyeno Aroni anawauza kuti: “Tengani ndolo zagolide+ zimene avala akazi anu, ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mubwere nazo kwa ine.”