Ekisodo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako iye analandira golideyo kuchokera kwa anthuwo ndipo pogwiritsa ntchito chosemera, anapanga fano* la mwana wa ngʼombe.+ Zitatero iwo anayamba kunena kuti: “Uyu ndi Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:4 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44
4 Kenako iye analandira golideyo kuchokera kwa anthuwo ndipo pogwiritsa ntchito chosemera, anapanga fano* la mwana wa ngʼombe.+ Zitatero iwo anayamba kunena kuti: “Uyu ndi Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo.”+