Ekisodo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka mʼmamawa kwambiri nʼkuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zamgwirizano. Atatero, iwo anakhala pansi ndipo anadya ndi kumwa. Kenako anaimirira nʼkuyamba kusangalala.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:6 Nsanja ya Olonda,3/1/1995, tsa. 16
6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka mʼmamawa kwambiri nʼkuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zamgwirizano. Atatero, iwo anakhala pansi ndipo anadya ndi kumwa. Kenako anaimirira nʼkuyamba kusangalala.+