Ekisodo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndisiye kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize, koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:10 Nsanja ya Olonda,10/15/2010, ptsa. 5-6
10 Ndisiye kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize, koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+