Ekisodo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose atayandikira msasawo nʼkuona mwana wa ngʼombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wake unayaka ndipo anaponya pansi miyala ija nʼkuiswa ali mʼmunsi mwa phiri.+
19 Mose atayandikira msasawo nʼkuona mwana wa ngʼombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wake unayaka ndipo anaponya pansi miyala ija nʼkuiswa ali mʼmunsi mwa phiri.+