Ekisodo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anatenga mwana wa ngʼombe amene iwo anapanga nʼkumuwotcha pamoto kenako anamupera kuti akhale fumbi.+ Atatero anamwaza fumbilo pamadzi ndipo analamula Aisiraeli kuti amwe.+
20 Ndiyeno anatenga mwana wa ngʼombe amene iwo anapanga nʼkumuwotcha pamoto kenako anamupera kuti akhale fumbi.+ Atatero anamwaza fumbilo pamadzi ndipo analamula Aisiraeli kuti amwe.+