-
Ekisodo 32:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Mose anaona kuti anthuwo akuchita zinthu motayirira, chifukwa Aroni sanawaletse ndipo anachita zinthu zochititsa manyazi pamaso pa adani awo.
-