Ekisodo 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Mose anakaima pageti la msasawo ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo Alevi onse anapita kwa Mose.
26 Ndiyeno Mose anakaima pageti la msasawo ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo Alevi onse anapita kwa Mose.