Ekisodo 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero Mose anati: “Dziyeretseni* kuti mutumikire Yehova lero, chifukwa aliyense wa inu waukira mwana wake ndi mʼbale wake+ ndipo lero Mulungu akudalitsani.”+
29 Zitatero Mose anati: “Dziyeretseni* kuti mutumikire Yehova lero, chifukwa aliyense wa inu waukira mwana wake ndi mʼbale wake+ ndipo lero Mulungu akudalitsani.”+