Ekisodo 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Mose anabwerera kwa Yehova nʼkunena kuti: “Anthuwa achita tchimo lalikulu. Adzipangira mulungu wagolide!+
31 Ndiyeno Mose anabwerera kwa Yehova nʼkunena kuti: “Anthuwa achita tchimo lalikulu. Adzipangira mulungu wagolide!+