Ekisodo 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati mukufuna akhululukireni tchimo lawo.+ Koma ngati simukufuna, chonde ndifufuteni mʼbuku lanu limene mwalemba.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:32 Nsanja ya Olonda,11/1/2012, tsa. 159/1/1987, tsa. 29
32 Ngati mukufuna akhululukireni tchimo lawo.+ Koma ngati simukufuna, chonde ndifufuteni mʼbuku lanu limene mwalemba.”+