Ekisodo 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho pita uwatsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku limene ndidzapereke chilango, ndidzawalanga chifukwa cha tchimo lawo.” Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:34 Ulosi wa Danieli, ptsa. 204-205
34 Choncho pita uwatsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku limene ndidzapereke chilango, ndidzawalanga chifukwa cha tchimo lawo.”