Ekisodo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mupite kudziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Koma ine sindidzayenda pakati panu, chifukwa ndinu anthu okanika+ ndipo ndingakufafanizeni panjira.”+
3 Mupite kudziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Koma ine sindidzayenda pakati panu, chifukwa ndinu anthu okanika+ ndipo ndingakufafanizeni panjira.”+