Ekisodo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aisiraeli kuti, ‘Inu ndinu anthu okanika.+ Ndingathe kulowa pakati panu nʼkukufafanizani mʼkanthawi kochepa.+ Choncho musavale zodzikongoletsera pamene ndikuganizira zoti ndikuchiteni.’”
5 Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aisiraeli kuti, ‘Inu ndinu anthu okanika.+ Ndingathe kulowa pakati panu nʼkukufafanizani mʼkanthawi kochepa.+ Choncho musavale zodzikongoletsera pamene ndikuganizira zoti ndikuchiteni.’”