-
Ekisodo 33:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Mose akamapita kuchihemako, munthu aliyense ankaimirira pakhomo la tenti yake nʼkumayangʼanitsitsa Mose mpaka atalowa mʼchihemacho.
-