Ekisodo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Mose anauza Yehova kuti: “Inu mukundiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa,’ koma simunandidziwitse amene mudzamʼtume kuti ndipite naye. Komanso mwanena kuti, ‘Ndikukudziwa bwino ndi dzina lako lomwe,* ndipo ndakukomera mtima.’
12 Tsopano Mose anauza Yehova kuti: “Inu mukundiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa,’ koma simunandidziwitse amene mudzamʼtume kuti ndipite naye. Komanso mwanena kuti, ‘Ndikukudziwa bwino ndi dzina lako lomwe,* ndipo ndakukomera mtima.’