Ekisodo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati simupita nafe, kodi anthu adziwa bwanji kuti ine ndi anthu anuwa mwatikomera mtima? Koma mukapita nafe+ zisonyeza kuti ine ndi anthu anuwa mwatisiyanitsa ndi anthu ena onse amene ali padziko lapansi.”+
16 Ngati simupita nafe, kodi anthu adziwa bwanji kuti ine ndi anthu anuwa mwatikomera mtima? Koma mukapita nafe+ zisonyeza kuti ine ndi anthu anuwa mwatisiyanitsa ndi anthu ena onse amene ali padziko lapansi.”+