-
Ekisodo 33:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Yehova anapitiriza kuuza Mose kuti: “Ndichitanso zimene wapemphazi, chifukwa ndakukomera mtima ndipo ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe.”
-