Ekisodo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse, ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kumukomera mtima ndidzamukomera mtima, ndipo amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2019, tsa. 26 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 4
19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse, ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kumukomera mtima ndidzamukomera mtima, ndipo amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo.”+