Ekisodo 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukamapereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.+ Musamasunge nsembe ya chikondwerero cha Pasika mpaka mʼmawa.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:25 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, tsa. 12
25 Mukamapereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.+ Musamasunge nsembe ya chikondwerero cha Pasika mpaka mʼmawa.+