Ekisodo 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu onse aluso*+ pakati panu abwere ndipo adzapange zinthu zonse zimene Yehova walamula.