-
Ekisodo 35:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Adzapange chihema ndi nsalu yoyala pachihemacho, chophimba chake, ngowe zake, mafelemu ake, ndodo zake, zipilala zake ndi zitsulo zake zokhazikapo mafelemu ndi zipilala.
-