-
Ekisodo 35:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndipo onse amene anali ndi ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri, nsalu zabwino kwambiri, ubweya wa mbuzi, zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira ndi zikopa za akatumbu, anabwera nazo.
-