Ekisodo 35:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amuna ndi akazi onse amene anali ndi mtima wofunitsitsa anapereka kenakake kuti kathandize pa ntchito imene Yehova analamula kudzera mwa Mose. Aisiraeli anabweretsa zinthu zimenezi ngati nsembe yaufulu kwa Yehova.+
29 Amuna ndi akazi onse amene anali ndi mtima wofunitsitsa anapereka kenakake kuti kathandize pa ntchito imene Yehova analamula kudzera mwa Mose. Aisiraeli anabweretsa zinthu zimenezi ngati nsembe yaufulu kwa Yehova.+