Ekisodo 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Mose anauza Aisiraeli kuti: “Yehova wasankha Bezaleli, mwana wamwamuna wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda.+
30 Kenako Mose anauza Aisiraeli kuti: “Yehova wasankha Bezaleli, mwana wamwamuna wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda.+