-
Ekisodo 35:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Iye wawapatsa luso*+ kuti agwire ntchito zonse. Wawapatsa luso lopeta nsalu komanso luso loluka nsalu ndi ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri, nsalu zabwino kwambiri ndi luso lowomba nsalu. Amuna amenewa adzagwira ntchito iliyonse komanso kukonza kapangidwe ka zinthu zosiyanasiyana.”
-