Ekisodo 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Bezaleli adzagwire ntchito limodzi ndi Oholiabu komanso mwamuna aliyense waluso* amene Yehova wamupatsa nzeru ndi kuzindikira kuti adziwe mmene angagwirire ntchito zonse zopatulika mogwirizana ndi zimene Yehova walamula.”+
36 “Bezaleli adzagwire ntchito limodzi ndi Oholiabu komanso mwamuna aliyense waluso* amene Yehova wamupatsa nzeru ndi kuzindikira kuti adziwe mmene angagwirire ntchito zonse zopatulika mogwirizana ndi zimene Yehova walamula.”+