-
Ekisodo 36:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anaika zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu imodzi, ndipo anaikanso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu inayo kuti zikhale moyangʼanizana pamalo olumikizirana.
-