-
Ekisodo 36:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiyeno katani imeneyi anaipangira zipilala 4 za mtengo wa mthethe ndipo anazikuta ndi golide. Anapanganso tizitsulo tagolide tokolowekapo katani komanso zitsulo 4 zasiliva zokhazikapo zipilalazo.
-