-
Ekisodo 36:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Anapanganso zipilala zake 5 ndi tizitsulo take tokolowekapo nsalu yotchingayo. Pamwamba pa zipilalazo anakutapo ndi golide komanso tizitsulo take tolumikizira anatikuta ndi golide. Koma zitsulo zake 5 zokhazikapo zipilalazo zinali zakopa.
-