-
Ekisodo 37:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mphindi imodzi inali pansi pa nthambi zake ziwiri zoyambirira. Mphindi ina inalinso pansi pa nthambi zake ziwiri, ndipo mphindi inanso inali pansi pa nthambi zinanso ziwiri. Zinali choncho ndi nthambi 6 zotuluka muthunthu la choikapo nyale.
-