Ekisodo 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anapanganso nyanga mʼmakona ake 4. Nyanga zake anazipangira kumodzi ndi guwalo.* Atatero anakuta guwalo ndi kopa.*+
2 Anapanganso nyanga mʼmakona ake 4. Nyanga zake anazipangira kumodzi ndi guwalo.* Atatero anakuta guwalo ndi kopa.*+