Ekisodo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake chakopa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito magalasi odziyangʼanira* a azimayi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:8 Nsanja ya Olonda,4/1/2015, tsa. 15
8 Kenako anapanga beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake chakopa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito magalasi odziyangʼanira* a azimayi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.