Ekisodo 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anapanga bwalo.+ Kumbali yakumʼmwera ya bwalolo anapangako mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo unali mamita 45 mulitali mwake.+
9 Ndiyeno anapanga bwalo.+ Kumbali yakumʼmwera ya bwalolo anapangako mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo unali mamita 45 mulitali mwake.+