-
Ekisodo 38:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kumbali yakumpoto, mpandawo unali mamita 45 mulitali mwake. Zipilala zake 20 ndi zitsulo 20 zokhazikapo zipilalazo zinali zakopa. Tizitsulo ta zipilala tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.
-