Ekisodo 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mose analamula kuti awerengere zinthu zonse zimene anagwiritsa ntchito popanga chihema, kapena kuti chihema cha Umboni.+ Alevi ndi amene anachita zimenezi+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe.
21 Mose analamula kuti awerengere zinthu zonse zimene anagwiritsa ntchito popanga chihema, kapena kuti chihema cha Umboni.+ Alevi ndi amene anachita zimenezi+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe.