-
Ekisodo 38:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Masekeli 1,775 anawagwiritsa ntchito popangira tizitsulo ta zipilala tokolowekapo nsalu ndi kukutira pamwamba pa zipilalazo. Atatero analumikiza zipilalazo.
-