-
Ekisodo 39:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Anasula golide kukhala wopyapyala kwambiri, ndipo anamulezaleza kukhala ngati tizingwe kuti apetere limodzi ndi ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wabwino kwambiri.
-