Ekisodo 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anaika miyala ya onekisi mʼzoikamo zagolide. Pamiyalayo analembapo mayina a ana a Isiraeli mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+
6 Ndiyeno anaika miyala ya onekisi mʼzoikamo zagolide. Pamiyalayo analembapo mayina a ana a Isiraeli mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+