Ekisodo 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akachipinda pakati chinali chofanana mbali zonse 4. Chovala pachifuwacho anachipanga kuti akachipinda pakati, mulitali mwake chizikhala masentimita 22* ndiponso mulifupi mwake masentimita 22.
9 Akachipinda pakati chinali chofanana mbali zonse 4. Chovala pachifuwacho anachipanga kuti akachipinda pakati, mulitali mwake chizikhala masentimita 22* ndiponso mulifupi mwake masentimita 22.