-
Ekisodo 39:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndipo mzere wa 4 unali ndi miyala ya kulusolito, onekisi ndi yade. Anaiika mʼzoikamo zake zagolide.