-
Ekisodo 39:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Miyalayo anaiika mogwirizana ndi mayina a ana 12 a Isiraeli. Mwala uliwonse analembapo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo ndipo mwala uliwonse unali ndi dzina limodzi mwa mayina a mafuko 12.
-