-
Ekisodo 39:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Anapanganso zoikamo miyala ziwiri zagolide ndi mphete ziwiri zagolide, ndipo anaika mphete ziwirizo mʼmakona awiri a chovala pachifuwacho.
-